Skip to content
Opens in a new window
Listen to this chapter • 0:41

[1] Inu Yehova, mtima wanga siwodzikuza, maso anga siwonyada; sinditengeteka mtima ndi zinthu zapamwamba ndi zodabwitsa.

[2] Koma moyo wanga ndawutontholetsa ndi kuwukhalitsa chete ngati mwana amene amayi ake amuletsa kuyamwa, moyo wanga mʼkati mwanga uli ngati mwana amene amuletsa kuyamwa.

[3] Yembekeza Yehova, iwe Israeli, kuyambira tsopano mpaka muyaya.

Masalimo — Chapters